Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kodi simukudziwa kuti Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka ufumu kwa Davide kuti azilamulira Isiraeli mpaka kalekale?+ Simukudziwa kodi kuti anaupereka kwa iye ndi ana ake+ pochita naye pangano la mchere?*+

  • Salimo 89:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu anati: “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga.+

      Ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga kuti:+

       4 ‘Ndidzachititsa kuti mbadwa* zako zikhalepo mpaka kalekale,+

      Ndipo ndidzachititsa kuti ufumu* wako ukhalepo ku mibadwo yonse.’”+ (Selah)

  • Salimo 132:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova walumbira kwa Davide.

      Ndithudi sadzalephera kukwaniritsa mawu ake akuti:

      “Ndidzaika pampando wako wachifumu

      Mmodzi wa ana ako.*+

  • Yeremiya 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene ndidzaike mfumu yolungama pampando wachifumu yochokera mʼbanja lachifumu la Davide.*+ Mfumuyo idzalamulira mʼdzikoli+ ndipo idzachita zinthu mwanzeru, motsatira malamulo komanso mwachilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena