Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 64:2, 3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndibiseni ku ziwembu zachinsinsi za anthu oipa,+

      Kwa gulu la anthu ochita zoipa.

       3 Iwo amanola lilime lawo ngati lupanga.

      Amakonzekera kuponya mawu awo opweteka ngati mivi,

  • Yesaya 54:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chida chilichonse chimene chidzapangidwe kuti chikuvulaze sichidzapambana,+

      Ndipo lilime lililonse limene lidzalimbane nawe pamlandu udzalitsutsa.

      Ichi ndi cholowa cha atumiki a Yehova,

      Ndipo chilungamo chawo nʼchochokera kwa ine,” akutero Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena