Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komanso pa nthawi ya zisangalalo+ zanu, monga pa zikondwerero+ zanu ndi kumayambiriro kwa miyezi, muziliza malipenga popereka nsembe zanu zopsereza+ ndi zamgwirizano.+ Kulira kwa malipengawo kudzachititsa kuti Mulungu akukumbukireni. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.”+

  • 1 Mbiri 15:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Aisiraeli onse ankapita limodzi ndi likasa la pangano la Yehova akufuula mokondwera+ ndiponso akuliza nyanga za nkhosa ndi malipenga.+ Iwo ankaimbanso mokweza zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze.+

  • 2 Mbiri 29:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako Hezekiya analamula kuti apereke nsembe yopsereza paguwa lansembe.+ Atayamba kupereka nsembeyo, anayamba kuimba nyimbo ya Yehova ndiponso malipenga motsatira zipangizo zoimbira za Davide mfumu ya Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena