Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ganizirani za akhwangwala: Iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nkhokwe kapena nyumba yosungiramo zinthu, koma Mulungu amawadyetsa.+ Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?+
24 Ganizirani za akhwangwala: Iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nkhokwe kapena nyumba yosungiramo zinthu, koma Mulungu amawadyetsa.+ Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?+