Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mauta a anthu amphamvu awonongedwa,

      Koma ofooka apatsidwa mphamvu.+

  • 2 Samueli 22:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Mudzandipatsa mphamvu kuti ndithe kumenya nkhondo;+

      Mudzachititsa kuti adani anga agonje.+

  • Yesaya 40:29-31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa

      Ndipo munthu amene alibe mphamvu amamupatsa mphamvu zambiri.+

      30 Anyamata adzatopa nʼkufooka,

      Ndipo amuna achinyamata adzapunthwa nʼkugwa,

      31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu.

      Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+

      Adzathamanga koma osafooka.

      Adzayenda koma osatopa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena