Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,

      Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+

      Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+

  • Aroma 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma chifukwa chakuti sukufuna kusintha, ndipo ukusonyeza mtima wosalapa, Mulungu adzakulanga ndithu pa tsiku la mkwiyo wake akamadzaulula chiweruzo chake cholungama.+

  • Chivumbulutso 11:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma mitundu ya anthu inakwiya ndipo inunso munasonyeza mkwiyo wanu. Ndiye nthawi yoikidwiratu inafika yoti akufa aweruzidwe nʼkupereka mphoto+ kwa akapolo anu aneneri+ komanso kwa oyera ndi amene akuopa dzina lanu, olemekezeka ndi onyozeka omwe. Komanso nthawi yoti muwononge amene akuwononga dziko lapansi.”+

  • Chivumbulutso 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno ndinaona chilombo, mafumu a dziko lapansi ndi asilikali awo atasonkhana pamodzi kuti amenyane ndi amene anakwera pahatchi uja ndi gulu lake lankhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena