Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Litamandike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+

      Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+

      Ame! Ame!

  • Salimo 86:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mitundu yonse ya anthu imene munapanga

      Idzabwera nʼkudzagwada pamaso panu, inu Yehova,+

      Ndipo idzalemekeza dzina lanu.+

  • Yesaya 59:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Amene ali kolowera dzuwa adzaopa dzina la Yehova,

      Ndipo amene ali kotulukira dzuwa adzaopa ulemerero wake,

      Chifukwa iye adzabwera ngati mtsinje wothamanga,

      Umene ukuyendetsedwa ndi mzimu wa Yehova.

  • Malaki 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Kuchokera kotulukira dzuwa kukafika kumene limalowera,* dzina langa lidzakwezeka pakati pa anthu a mitundu ina.+ Kulikonse anthu azidzapereka nsembe zautsi ndiponso nsembe zina ngati mphatso zovomerezeka polemekeza dzina langa. Adzachita izi chifukwa dzina langa lidzakwezeka pakati pa anthu a mitundu inawo,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena