Salimo 132:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe mʼmalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa limene likuimira mphamvu zanu.+ 9 Ansembe anu avale chilungamo,Ndipo okhulupirika anu afuule mosangalala.
8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe mʼmalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa limene likuimira mphamvu zanu.+ 9 Ansembe anu avale chilungamo,Ndipo okhulupirika anu afuule mosangalala.