Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.” Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+ Yesaya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa kwa ife kwabadwa mwana,+Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,Ndipo ulamuliro* udzakhala paphewa pake.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wamuyaya, Kalonga Wamtendere. Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+
6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”
8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+
6 Chifukwa kwa ife kwabadwa mwana,+Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,Ndipo ulamuliro* udzakhala paphewa pake.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wamuyaya, Kalonga Wamtendere.
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+