Luka 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera udzafika pa iwe+ ndipo mphamvu ya Wamʼmwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechi amene adzabadweyo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+ Luka 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa lero, mumzinda wa Davide+ mwabadwa mpulumutsi wanu,+ amene ndi Khristu Ambuye.+
35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera udzafika pa iwe+ ndipo mphamvu ya Wamʼmwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechi amene adzabadweyo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+