Yobu 38:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndi ndani anaika nzeru mʼmitambo,*+Kapena ndi ndani anachititsa kuti zinthu zakuthambo zikhale zozindikira?*+ Miyambo 3:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anayala maziko a dziko lapansi mwanzeru.+ Anakhazikitsa kumwamba mozindikira.+ 20 Chifukwa chakuti iye amadziwa zinthu, anagawa madzi akuyaNdipo kumwamba kwa mitambo kunagwetsa mame.+
36 Ndi ndani anaika nzeru mʼmitambo,*+Kapena ndi ndani anachititsa kuti zinthu zakuthambo zikhale zozindikira?*+
19 Yehova anayala maziko a dziko lapansi mwanzeru.+ Anakhazikitsa kumwamba mozindikira.+ 20 Chifukwa chakuti iye amadziwa zinthu, anagawa madzi akuyaNdipo kumwamba kwa mitambo kunagwetsa mame.+