Salimo 64:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndibiseni ku ziwembu zachinsinsi za anthu oipa,+Kwa gulu la anthu ochita zoipa. Salimo 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amafufuza njira zatsopano zochitira zinthu zoipa.Mwachinsinsi amakonza njira zochitira ziwembu zawo mochenjera.+Zimene munthu aliyense akuganiza mumtima mwake, nʼzovuta kuzimvetsa.
6 Amafufuza njira zatsopano zochitira zinthu zoipa.Mwachinsinsi amakonza njira zochitira ziwembu zawo mochenjera.+Zimene munthu aliyense akuganiza mumtima mwake, nʼzovuta kuzimvetsa.