2 Samueli 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Davide anauzidwa kuti: “Ahitofeli nayenso ali mʼgulu la anthu amene akukonza chiwembu+ ndi Abisalomu.”+ Davide atamva zimenezi anati: “Chonde Yehova,+ chititsani kuti malangizo a Ahitofeli akhale opusa.”+ Salimo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musandipereke kwa adani anga,+Chifukwa mboni zabodza zikundinamizira mlandu,+Ndipo akundiopseza kuti andichitira zachiwawa.
31 Kenako Davide anauzidwa kuti: “Ahitofeli nayenso ali mʼgulu la anthu amene akukonza chiwembu+ ndi Abisalomu.”+ Davide atamva zimenezi anati: “Chonde Yehova,+ chititsani kuti malangizo a Ahitofeli akhale opusa.”+
12 Musandipereke kwa adani anga,+Chifukwa mboni zabodza zikundinamizira mlandu,+Ndipo akundiopseza kuti andichitira zachiwawa.