Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mkwiyo wanga wayatsa moto+Umene udzayaka mpaka kukafika pansi penipeni pa Manda,*+Ndipo udzapsereza dziko lapansi ndi zokolola zake,Komanso udzayatsa maziko a mapiri. Salimo 110:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova adzakhala kudzanja lako lamanja.+Iye adzaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wake.+ Malaki 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ngʼanjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi. Pa tsikulo iwo adzawonongedwa moti sipadzatsala mizu kapena nthambi zawo,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
22 Mkwiyo wanga wayatsa moto+Umene udzayaka mpaka kukafika pansi penipeni pa Manda,*+Ndipo udzapsereza dziko lapansi ndi zokolola zake,Komanso udzayatsa maziko a mapiri.
4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ngʼanjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi. Pa tsikulo iwo adzawonongedwa moti sipadzatsala mizu kapena nthambi zawo,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.