Salimo 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene ndinakhala chete osaulula machimo anga, mafupa anga anafooka, chifukwa ndinkavutika mumtima mwanga tsiku lonse.+ Salimo 102:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa masiku a moyo wanga akuzimiririka ngati utsi,Ndipo mafupa anga akutentha kwambiri ngati ngʼanjo.+ Salimo 102:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa chakuti ndikubuula mokweza mawu,+Ndangotsala mafupa okhaokha.+
3 Pamene ndinakhala chete osaulula machimo anga, mafupa anga anafooka, chifukwa ndinkavutika mumtima mwanga tsiku lonse.+
3 Chifukwa masiku a moyo wanga akuzimiririka ngati utsi,Ndipo mafupa anga akutentha kwambiri ngati ngʼanjo.+