Salimo 102:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa cha kuusa moyo kwanga,+Thupi langa langotsala mafupa okhaokha.+