Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Komanso pamene Abisalomu ankapereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ wa ku Gilo, mlangizi wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Anthu amene anagwirizana ndi Abisalomu pa chiwembuchi anapitiriza kuwonjezeka.+

  • Yobu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Anzanga onse apamtima akudana nane,+

      Ndipo amene ndinkawakonda anditembenukira.+

  • Salimo 55:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chifukwa amene akundinyoza si mdani.+

      Akanakhala mdani ndikanapirira.

      Amene wandiukira si munthu wodana nane kwambiri.

      Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.

      13 Koma ndi iwe, munthu ngati ine ndemwe,*+

      Mnzanga weniweni amene ndikumudziwa bwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena