Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera. Miyambo 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mabala ovulazidwa ndi mnzako amakhala okhulupirika,+Koma makisi a munthu* amene amadana nawe amakhala ambiri.*
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.
6 Mabala ovulazidwa ndi mnzako amakhala okhulupirika,+Koma makisi a munthu* amene amadana nawe amakhala ambiri.*