Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+

      Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.

      Akuyangʼana mʼmawindo,

      Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo.

  • Nyimbo ya Solomo 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mpaka kunja kutayamba kuwomba kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka,

      Bwerera mwamsanga iwe wachikondi wanga,

      Kwera mapiri amene akutilekanitsa,* ngati insa+ komanso ngati mphoyo yaingʼono.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena