Nyimbo ya Solomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.Akuyangʼana mʼmawindo,Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo. Nyimbo ya Solomo 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Fulumira wachikondi wanga,Thamanga ngati insa+Kapena ngati mphoyo yaingʼonoPamapiri amaluwa onunkhira.”
9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.Akuyangʼana mʼmawindo,Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo.
14 “Fulumira wachikondi wanga,Thamanga ngati insa+Kapena ngati mphoyo yaingʼonoPamapiri amaluwa onunkhira.”