Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 42:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza,

      Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+

      Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+

      Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+

  • Yesaya 61:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Mzimu wa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, uli pa ine,+

      Chifukwa Yehova anandidzoza kuti ndilengeze uthenga wabwino kwa anthu ofatsa.+

      Anandituma kuti ndikamange mabala a anthu osweka mtima,

      Kuti ndilengeze za ufulu kwa anthu amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,

      Komanso kuti maso a akaidi adzatsegulidwa.+

  • Afilipi 2:5-7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Khalani ndi maganizo amenenso Khristu Yesu anali nawo.+ 6 Ngakhale kuti iye ankaoneka ngati Mulungu,+ sanaganizirepo zoti ayese kulanda udindo wa Mulungu kuti akhale wofanana naye.+ 7 Ayi sanachite zimenezo, koma anasiya zonse zimene anali nazo nʼkukhala ngati kapolo+ ndipo anakhala munthu.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena