Yesaya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri. Yeremiya 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anauza mneneri Yeremiya zokhudza kubwera kwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo kudzaukira dziko la Iguputo. Iye anati:+
19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri.
13 Yehova anauza mneneri Yeremiya zokhudza kubwera kwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo kudzaukira dziko la Iguputo. Iye anati:+