Salimo 85:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munakhululukira anthu anu zolakwa zawo.Munawakhululukira* machimo awo onse.+ (Selah) 3 Munabweza mkwiyo wanu wonse,Ndipo simunasonyeze mkwiyo wanu waukulu.+ Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku limenelo ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani, inu YehovaChifukwa ngakhale munandikwiyira,Mkwiyo wanu unachepa pangʼonopangʼono ndipo munanditonthoza.+
2 Munakhululukira anthu anu zolakwa zawo.Munawakhululukira* machimo awo onse.+ (Selah) 3 Munabweza mkwiyo wanu wonse,Ndipo simunasonyeze mkwiyo wanu waukulu.+
12 Pa tsiku limenelo ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani, inu YehovaChifukwa ngakhale munandikwiyira,Mkwiyo wanu unachepa pangʼonopangʼono ndipo munanditonthoza.+