2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼchaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ nʼkutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani+ ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+ Yesaya 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mu Efuraimu simudzakhalanso mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+Ndipo mu Damasiko simudzakhalanso ufumu.+Anthu amene adzatsale mu SiriyaAdzakhala ngati ulemerero wa Aisiraeli,”* akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
6 Mʼchaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ nʼkutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani+ ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+
3 Mu Efuraimu simudzakhalanso mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+Ndipo mu Damasiko simudzakhalanso ufumu.+Anthu amene adzatsale mu SiriyaAdzakhala ngati ulemerero wa Aisiraeli,”* akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.