Yesaya 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mu Efuraimu mulibenso mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri,+ ndipo mu Damasiko mulibenso ufumu.+ Ulemerero wa anthu otsala mu Siriya udzatha ngati ulemerero wa ana a Isiraeli,” akutero Yehova wa makamu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Yesaya 1, tsa. 196
3 Mu Efuraimu mulibenso mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri,+ ndipo mu Damasiko mulibenso ufumu.+ Ulemerero wa anthu otsala mu Siriya udzatha ngati ulemerero wa ana a Isiraeli,” akutero Yehova wa makamu.+