Yesaya 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mu Efuraimu simudzakhalanso mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+Ndipo mu Damasiko simudzakhalanso ufumu.+Anthu amene adzatsale mu SiriyaAdzakhala ngati ulemerero wa Aisiraeli,”* akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Yesaya 1, tsa. 196
3 Mu Efuraimu simudzakhalanso mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+Ndipo mu Damasiko simudzakhalanso ufumu.+Anthu amene adzatsale mu SiriyaAdzakhala ngati ulemerero wa Aisiraeli,”* akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.