Levitiko 26:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, iwo akamadzakhala mʼdziko la adani awo, sindidzawakana mpaka kalekale+ kapena kunyansidwa nawo moti nʼkuwawonongeratu, zomwe zingaphwanye pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo. Yeremiya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova, ndilangizeni pondipatsa chiweruzo,Koma osati mutakwiya+ chifukwa mungandiwononge.+
44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, iwo akamadzakhala mʼdziko la adani awo, sindidzawakana mpaka kalekale+ kapena kunyansidwa nawo moti nʼkuwawonongeratu, zomwe zingaphwanye pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo.