Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+ Yoweli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wonse.+Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokweza.
7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+
12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wonse.+Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokweza.