Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova ali kutali ndi anthu oipa,Koma amamva pemphero la anthu olungama.+ 1 Yohane 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipotu ife sitikayikira*+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi zimene amafuna, amatimvera.+
14 Ndipotu ife sitikayikira*+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi zimene amafuna, amatimvera.+