Numeri 32:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ana a Rubeni anamanga mizinda ya Hesiboni,+ Eleyale,+ Kiriyataimu,+ Yeremiya 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ponena za Mowabu,+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Tsoka Nebo+ chifukwa wawonongedwa! Kiriyataimu+ wachititsidwa manyazi ndipo walandidwa. Malo othawirako otetezeka* achititsidwa manyazi ndipo awonongedwa.+
48 Ponena za Mowabu,+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Tsoka Nebo+ chifukwa wawonongedwa! Kiriyataimu+ wachititsidwa manyazi ndipo walandidwa. Malo othawirako otetezeka* achititsidwa manyazi ndipo awonongedwa.+