Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+ Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+ Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+