-
Deuteronomo 28:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yehova adzachititsa kuti adani anu akugonjetseni.+ Popita kukawaukira mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa mudzadutsa njira zosiyanasiyana 7. Mafumu onse a dziko lapansi adzachita mantha akadzaona zinthu zoipa zimene zakuchitikirani.+ 26 Mitembo yanu idzakhala chakudya cha mbalame zonse zouluka mumlengalenga ndi zilombo zoyenda panthaka, ndipo sipadzapezeka woziopseza.+
-