Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+

  • Deuteronomo 28:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani.

  • Yesaya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tamverani! Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,

      Akuchotsa mu Yerusalemu ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo,

      Monga mkate ndi madzi.+

  • Ezekieli 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Uzidzamwa madzi ochita kuyeza, ndipo uzidzamwa makapu awiri okha.* Uzidzamwa madziwo nthawi yofanana tsiku lililonse.

  • Ezekieli 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzachititsa kuti chakudya chisowe* mu Yerusalemu.+ Anthu azidzadya chakudya chochita kuyeza ndipo adzachidya ali ndi nkhawa yaikulu.+ Azidzamwa madzi ochita kuyeza ali ndi mantha aakulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena