Ekisodo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Upange guwa lansembe zofukiza.+ Ulipange ndi matabwa amthethe.+ 1 Mafumu 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Solomo anapanga zinthu zonse zapanyumba ya Yehova. Anapanga guwa lansembe+ lagolide komanso tebulo yagolide+ yoikapo mkate wachionetsero. Chivumbulutso 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu.
48 Solomo anapanga zinthu zonse zapanyumba ya Yehova. Anapanga guwa lansembe+ lagolide komanso tebulo yagolide+ yoikapo mkate wachionetsero.
3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu.