2 Mafumu 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno mpanda wa mzindawo unabooledwa+ ndipo asilikali onse anathawa usiku kudzera pageti limene linali pakati pa makoma awiri, pafupi ndi munda wa mfumu. Akasidi anali atazungulira mzindawo ndipo mfumu inayamba kuthawa kulowera cha ku Araba.+ Yeremiya 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi asilikali onse ataona adaniwo, anathawira+ kunja kwa mzinda usiku. Iwo anadzera njira yakumunda wa mfumu nʼkukadutsa pageti limene linali pakati pa makoma awiri ndipo anapitiriza kuthawa kulowera ku Araba.+
4 Ndiyeno mpanda wa mzindawo unabooledwa+ ndipo asilikali onse anathawa usiku kudzera pageti limene linali pakati pa makoma awiri, pafupi ndi munda wa mfumu. Akasidi anali atazungulira mzindawo ndipo mfumu inayamba kuthawa kulowera cha ku Araba.+
4 Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi asilikali onse ataona adaniwo, anathawira+ kunja kwa mzinda usiku. Iwo anadzera njira yakumunda wa mfumu nʼkukadutsa pageti limene linali pakati pa makoma awiri ndipo anapitiriza kuthawa kulowera ku Araba.+