Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+

      Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,

      Ari+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete.

      Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,

      Kiri+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete.

  • Yeremiya 48:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ponena za Mowabu,+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti:

      “Tsoka Nebo+ chifukwa wawonongedwa!

      Kiriyataimu+ wachititsidwa manyazi ndipo walandidwa.

      Malo othawirako otetezeka* achititsidwa manyazi ndipo awonongedwa.+

  • Amosi 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Yehova wanena kuti,

      ‘“Popeza Mowabu anandigalukira mobwerezabwereza,*+ sindidzamusinthira chigamulo changa.

      Chifukwa anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena