Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso mʼdziko lake, chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa* cha Iguputo+ mpaka kumtsinje wa Firate.+

  • Yeremiya 46:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo+ wonena za gulu la asilikali a Farao Neko,+ mfumu ya Iguputo, amene anagonjetsedwa ndi Nebukadinezara* mfumu ya Babulo ku Karikemisi, mʼmbali mwa mtsinje wa Firate. Anagonjetsedwa ndi mfumu imeneyi mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Uthengawo unali wakuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena