Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya ananditsekereza kwa masiku 21. Ndiyeno Mikayeli,*+ mmodzi wa akalonga aakulu,* anabwera kudzandithandiza. Pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pomwepo pafupi ndi mafumu a Perisiya.

  • Yuda 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma pamene Mikayeli,+ mkulu wa angelo,+ anasemphana maganizo ndi Mdyerekezi ndipo anakangana naye za mtembo wa Mose,+ sanayese nʼkomwe kumuweruza komanso kumunyoza,+ mʼmalomwake anati: “Yehova* akudzudzule.”+

  • Chivumbulutso 12:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo kumwamba kunabuka nkhondo: Mikayeli*+ ndi angelo ake anamenyana ndi chinjoka. Chinjokacho ndi angelo ake chinamenya nkhondo, 8 koma sanapambane* ndipo malo awo sanapezekenso kumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena