Ekisodo 12:50, 51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Choncho Aisiraeli onse anachita mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose ndi Aroni. Anachitadi zomwezo. 51 Pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa Aisiraeli onse* mʼdziko la Iguputo. Salimo 77:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+
50 Choncho Aisiraeli onse anachita mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose ndi Aroni. Anachitadi zomwezo. 51 Pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa Aisiraeli onse* mʼdziko la Iguputo.