Amosi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja nʼkumakhalamo.+Adzalima minda ya mpesa nʼkumwa vinyo wake.+Adzalimanso minda nʼkudya zipatso zake.’+ Zekariya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Mʼdzikolo mudzadzalidwa mbewu ya mtendere. Mpesa udzabala zipatso ndipo dziko lapansi lidzatulutsa zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ndipo ndidzachititsa kuti anthu otsala alandire zinthu zonsezi.+
14 Ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja nʼkumakhalamo.+Adzalima minda ya mpesa nʼkumwa vinyo wake.+Adzalimanso minda nʼkudya zipatso zake.’+
12 ‘Mʼdzikolo mudzadzalidwa mbewu ya mtendere. Mpesa udzabala zipatso ndipo dziko lapansi lidzatulutsa zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ndipo ndidzachititsa kuti anthu otsala alandire zinthu zonsezi.+