Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 34:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Chifukwa Yehova wakwiyira mitundu yonse ya anthu,+

      Ndipo wapsera mtima asilikali awo onse.+

      Iye adzawawononga

      Ndipo adzawapha.+

  • Yoweli 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndidzasonkhanitsanso anthu a mitundu yonse,

      Nʼkuwabweretsa mʼchigwa cha Yehosafati.*

      Ndipo ndidzawaweruza kumeneko,+

      Mʼmalo mwa anthu anga ndiponso cholowa changa, Isiraeli.

      Chifukwa anamwaza Aisiraeli pakati pa anthu a mitundu ina,

      Ndiponso anagawana dziko langa.+

  • Chivumbulutso 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu a dziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitse pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse.+

  • Chivumbulutso 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno ndinaona chilombo, mafumu a dziko lapansi ndi asilikali awo atasonkhana pamodzi kuti amenyane ndi amene anakwera pahatchi uja ndi gulu lake lankhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena