Ekisodo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musachite chigololo.+ Deuteronomo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musachite chigololo.+ Luka 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musachite chigololo,+ musaphe munthu,*+ musabe,+ musapereke umboni wabodza+ ndiponso lakuti, muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+ Aroma 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa malamulo onena kuti, “usachite chigololo,+ usaphe munthu,+ usabe,+ usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili mʼmawu awa akuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+
20 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musachite chigololo,+ musaphe munthu,*+ musabe,+ musapereke umboni wabodza+ ndiponso lakuti, muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+
9 Chifukwa malamulo onena kuti, “usachite chigololo,+ usaphe munthu,+ usabe,+ usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili mʼmawu awa akuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+