Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Petulo, atadzazidwa ndi mzimu woyera,+ anawayankha kuti:

      “Inu olamulira ndiponso akulu,

  • Machitidwe 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Bwanamkubwayo atagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti:

      “Ndikudziwa kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri. Choncho ndine wosangalala kulankhula podziteteza pa zimene akundinenerazi.+

  • Machitidwe 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsiku lotsatira, Agiripa ndi Berenike anabwera ndi ulemu waukulu wachifumu nʼkulowa mʼchipinda chimene anthu ankasonkhana. Anali ndi akuluakulu a asilikali komanso anthu otchuka amumzindawo ndipo Fesito atalamula, anabweretsa Paulo.

  • Machitidwe 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Paulo anati: “Wolemekezeka a Fesito, inetu sindinachite misala, koma ndikulankhula mawu a choonadi ndipo ndili bwinobwino.

  • Machitidwe 27:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Usiku wapitawu mngelo+ wa Mulungu wanga amene ndikumuchitira utumiki wopatulika, anaima pafupi ndi ine 24 nʼkunena kuti: ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara.+ Ndipo dziwa kuti chifukwa cha iwe, Mulungu apulumutsa anthu onse amene uli nawo pa ulendowu.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena