Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anthu adzakuperekani kuti mukazunzidwe+ ndipo adzakuphani.+ Anthu a mitundu yonse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Luka 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Yohane 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+
9 Kenako anthu adzakuperekani kuti mukazunzidwe+ ndipo adzakuphani.+ Anthu a mitundu yonse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+
21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+