Zekariya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+ Machitidwe 9:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero anagwa pansi ndipo anamva mawu akuti: “Saulo, Saulo, nʼchifukwa chiyani ukundizunza?” 5 Iye anafunsa kuti: “Mbuyanga, ndinu ndani kodi?” Anamuyankha kuti: “Ndine Yesu,+ amene ukumuzunza.+
8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+
4 Zitatero anagwa pansi ndipo anamva mawu akuti: “Saulo, Saulo, nʼchifukwa chiyani ukundizunza?” 5 Iye anafunsa kuti: “Mbuyanga, ndinu ndani kodi?” Anamuyankha kuti: “Ndine Yesu,+ amene ukumuzunza.+