Mateyu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chenjerani ndi anthu, chifukwa adzakutengerani kumakhoti aangʼono,+ ndipo adzakukwapulani+ mumasunagoge awo.+ Yohane 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu adzakuchotsani musunagoge.+ Ndipotu nthawi ikubwera pamene aliyense amene adzakupheni+ adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.
17 Chenjerani ndi anthu, chifukwa adzakutengerani kumakhoti aangʼono,+ ndipo adzakukwapulani+ mumasunagoge awo.+
2 Anthu adzakuchotsani musunagoge.+ Ndipotu nthawi ikubwera pamene aliyense amene adzakupheni+ adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.