Mateyu 10:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musatenge golide, siliva kapena kopa* mʼzikwama zanu za ndalama.+ 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo kapena malaya awiri* kapena nsapato kapenanso ndodo+ chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+ Luka 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anawauza kuti: “Musatenge kanthu pa ulendowu, kaya ndodo, thumba la chakudya, mkate, ndalama kapena malaya awiri.*+
9 Musatenge golide, siliva kapena kopa* mʼzikwama zanu za ndalama.+ 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo kapena malaya awiri* kapena nsapato kapenanso ndodo+ chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+
3 Iye anawauza kuti: “Musatenge kanthu pa ulendowu, kaya ndodo, thumba la chakudya, mkate, ndalama kapena malaya awiri.*+