Luka 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho muzikhala mʼnyumba imeneyo+ ndipo muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako nʼkupita kunyumba zina. 1 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi alipo msilikali amene amatumikira, koma nʼkumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwa mkaka wake? 1 Akorinto 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso Ambuye analamula kuti anthu amene amalalikira uthenga wabwino azipeza zofunika pa moyo kudzera mu uthenga wabwino.+
7 Choncho muzikhala mʼnyumba imeneyo+ ndipo muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako nʼkupita kunyumba zina.
7 Kodi alipo msilikali amene amatumikira, koma nʼkumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwa mkaka wake?
14 Komanso Ambuye analamula kuti anthu amene amalalikira uthenga wabwino azipeza zofunika pa moyo kudzera mu uthenga wabwino.+