Mateyu 24:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pa chifukwa chimenechi, inunso khalani okonzeka,+ chifukwa Mwana wa munthu adzabwera pa ola limene simukuliganizira. Mateyu 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho pitirizani kukhala maso+ chifukwa simukudziwa tsiku kapena ola lake.+ Chivumbulutso 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka, ndidzabwera ngati wakuba+ ndipo sudzadziwa ngakhale pangʼono ola limene ndidzafike kwa iwe.+
44 Pa chifukwa chimenechi, inunso khalani okonzeka,+ chifukwa Mwana wa munthu adzabwera pa ola limene simukuliganizira.
3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka, ndidzabwera ngati wakuba+ ndipo sudzadziwa ngakhale pangʼono ola limene ndidzafike kwa iwe.+