Yohane 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma inu simukukhulupirira, chifukwa si inu nkhosa zanga.+ 1 Yohane 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ife tinachokera kwa Mulungu. Amene amadziwa Mulungu amatimvera,+ koma amene sanachokere kwa Mulungu satimvera.+ Mmenemu ndi mmene timadziwira mawu ouziridwa oona kapena mawu ouziridwa abodza.+
6 Ife tinachokera kwa Mulungu. Amene amadziwa Mulungu amatimvera,+ koma amene sanachokere kwa Mulungu satimvera.+ Mmenemu ndi mmene timadziwira mawu ouziridwa oona kapena mawu ouziridwa abodza.+